Mateyu 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso mukamapemphera, musamachite zimene anthu achinyengo amachita.+ Chifukwa iwo amakonda kuima mʼmasunagoge ndi mumphambano za misewu ikuluikulu kuti anthu aziwaona.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 88 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 112/15/2009, ptsa. 15-167/15/1996, tsa. 610/1/1990, ptsa. 16-177/15/1990, tsa. 65/15/1987, tsa. 8
5 Komanso mukamapemphera, musamachite zimene anthu achinyengo amachita.+ Chifukwa iwo amakonda kuima mʼmasunagoge ndi mumphambano za misewu ikuluikulu kuti anthu aziwaona.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.
6:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 88 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 112/15/2009, ptsa. 15-167/15/1996, tsa. 610/1/1990, ptsa. 16-177/15/1990, tsa. 65/15/1987, tsa. 8