-
Mateyu 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ukamapemphera, usamanene mawu omweomwewo mobwerezabwereza ngati mmene anthu a mitundu ina amachitira. Iwo amaganiza kuti Mulungu awamvetsera akanena mawu ambirimbiri.
-