Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Nsanja ya Olonda,2/1/2004, ptsa. 14-167/15/1996, tsa. 19