Mateyu 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mukamasala kudya,+ siyani kuonetsa nkhope yachisoni ngati mmene anthu achinyengo aja amachitira. Iwo sasamalira nkhope* zawo kuti anthu ena adziwe kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 17
16 Mukamasala kudya,+ siyani kuonetsa nkhope yachisoni ngati mmene anthu achinyengo aja amachitira. Iwo sasamalira nkhope* zawo kuti anthu ena adziwe kuti akusala kudya.+ Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.