-
Mateyu 6:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 kuti anthu ena asadziwe kuti ukusala kudya, koma Atate wako wokha amene sungathe kuwaona. Ukatero Atate wako amene akuona zimene zikuchitika ngakhale kuti iweyo sungathe kuwaona, adzakubwezera.
-