-
Mateyu 6:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Komanso nʼchifukwa chiyani mukudera nkhawa nkhani ya zovala? Phunzirani mmene maluwa akutchire amakulira. Sagwira ntchito ndiponso sawomba nsalu.
-