-
Mateyu 6:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Chifukwa anthu a mitundu ina akufunafuna mwakhama zinthu zonsezi. Koma Atate wanu wakumwamba akudziwa kuti inuyo mumafunikira zinthu zonsezi.
-