-
Mateyu 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kapena ungauze bwanji mʼbale wako kuti, ‘Taima ndikuchotse kachitsotso mʼdiso lako,’ pamene iwe mʼdiso lako muli mtanda wa denga la nyumba?
-