-
Mateyu 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Wachinyengo iwe! Yamba wachotsa mtanda wa denga la nyumba umene uli mʼdiso lakowo. Ukatero udzatha kuona bwino moti udzakwanitsa kuchotsa kachitsotso mʼdiso la mʼbale wako.
-