Mateyu 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamapatse agalu zinthu zopatulika, kapena kuponyera nkhumba ngale zanu,+ kuopera kuti zingapondeponde ngalezo kenako zingatembenuke nʼkukukhadzulani. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:6 Yesu—Ndi Njira, tsa. 90 Galamukani!,2/8/2000, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 8
6 Musamapatse agalu zinthu zopatulika, kapena kuponyera nkhumba ngale zanu,+ kuopera kuti zingapondeponde ngalezo kenako zingatembenuke nʼkukukhadzulani.