Mateyu 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ngati inuyo mumadziwa kupereka mphatso zabwino kwa ana anu, ngakhale kuti ndinu oipa, kuli bwanji Atate wanu wakumwamba? Ndithudi, iye adzapereka mowolowa manja zinthu zabwino+ kwa amene akumupempha.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, ptsa. 18-195/15/1990, ptsa. 14-15
11 Choncho ngati inuyo mumadziwa kupereka mphatso zabwino kwa ana anu, ngakhale kuti ndinu oipa, kuli bwanji Atate wanu wakumwamba? Ndithudi, iye adzapereka mowolowa manja zinthu zabwino+ kwa amene akumupempha.+