Mateyu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chenjerani ndi aneneri abodza+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwa mitima yawo ali ngati mimbulu yolusa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:15 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 236/15/1987, tsa. 9
15 Chenjerani ndi aneneri abodza+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwa mitima yawo ali ngati mimbulu yolusa.+