Mateyu 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sikuti aliyense amene amanditchula kuti, ‘Ambuye, Ambuye,’ adzalowa Ufumu wakumwamba, koma yekhayo amene akuchita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:21 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 18 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 30-31
21 Sikuti aliyense amene amanditchula kuti, ‘Ambuye, Ambuye,’ adzalowa Ufumu wakumwamba, koma yekhayo amene akuchita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna.+