Mateyu 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Aliyense amene wamva mawu angawa koma osachita zimene wamvazo adzafanana ndi munthu wopusa amene anamanga nyumba yake pamchenga.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:26 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 29-312/15/2008, ptsa. 31-32
26 Aliyense amene wamva mawu angawa koma osachita zimene wamvazo adzafanana ndi munthu wopusa amene anamanga nyumba yake pamchenga.+