Mateyu 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yesu atamva zimenezo, anadabwa ndipo anauza amene ankamutsatira aja kuti: “Kunena zoona, mu Isiraeli sindinapezemo aliyense wachikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Nsanja ya Olonda,8/15/2002, tsa. 13
10 Yesu atamva zimenezo, anadabwa ndipo anauza amene ankamutsatira aja kuti: “Kunena zoona, mu Isiraeli sindinapezemo aliyense wachikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.+