Mateyu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ndikukuuzani kuti ambiri ochokera kumʼmawa ndi kumadzulo adzabwera nʼkukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu Ufumu wakumwamba,+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 93 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 25
11 Koma ndikukuuzani kuti ambiri ochokera kumʼmawa ndi kumadzulo adzabwera nʼkukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu Ufumu wakumwamba,+