Mateyu 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamene ana a Ufumuwo adzaponyedwa kunja kumdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 93 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 25