Mateyu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yesu ataona kuti gulu la anthu lamuzungulira, analamula kuti achoke nʼkupita kutsidya lina.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 8