Mateyu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno kunabwera mlembi nʼkumuuza kuti: “Mphunzitsi, ndikutsatirani kulikonse kumene mungapite.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:19 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 24
19 Ndiyeno kunabwera mlembi nʼkumuuza kuti: “Mphunzitsi, ndikutsatirani kulikonse kumene mungapite.”+