Mateyu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde ankalowetsa madzi mʼngalawamo, koma iye anali mʼtulo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:24 Nsanja ya Olonda,6/15/2015, tsa. 68/1/2012, tsa. 185/1/1987, tsa. 8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113
24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde ankalowetsa madzi mʼngalawamo, koma iye anali mʼtulo.+