Mateyu 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma iye anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka nʼkudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2021, tsa. 22 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113
26 Koma iye anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukuchita mantha chonchi, anthu achikhulupiriro chochepa inu?”+ Kenako anadzuka nʼkudzudzula mphepo ndi nyanjayo, ndipo panachita bata lalikulu.+
8:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2021, tsa. 22 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113