-
Mateyu 8:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Iye anaziuza kuti: “Pitani!” Choncho zinatuluka nʼkukalowa munkhumba zija. Nthawi yomweyo nkhumba zonsezo zinathamangira kuphedi nʼkulumphira mʼnyanja, ndipo zinafera mʼmadzimo.
-