Mateyu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anthu anamubweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pamachira. Yesu ataona chikhulupiriro chawo, anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima mwanawe! Machimo ako akhululukidwa.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 67 Nsanja ya Olonda,5/1/1986, ptsa. 8-9
2 Kumeneko anthu anamubweretsera munthu wakufa ziwalo, atagona pamachira. Yesu ataona chikhulupiriro chawo, anauza wakufa ziwaloyo kuti: “Limba mtima mwanawe! Machimo ako akhululukidwa.”+