Mateyu 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Afarisi ataona zimenezi anafunsa ophunzira ake kuti: “Nʼchifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi anthu okhometsa msonkho komanso ochimwa?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2017, ptsa. 16-17
11 Koma Afarisi ataona zimenezi anafunsa ophunzira ake kuti: “Nʼchifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi anthu okhometsa msonkho komanso ochimwa?”+