Mateyu 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ankawauza zimenezi, wolamulira wina anamuyandikira. Kenako anamugwadira nʼkunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale. Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+
18 Pamene ankawauza zimenezi, wolamulira wina anamuyandikira. Kenako anamugwadira nʼkunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale. Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+