Mateyu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, chifukwa mtsikanayu sanamwalire, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kumuseka monyoza. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 118 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 22
24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, chifukwa mtsikanayu sanamwalire, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kumuseka monyoza.