Mateyu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu akuchokera kumeneko, amuna awiri amene anali ndi vuto losaona+ anamutsatira akufuula kuti: “Mutichitire chifundo, Mwana wa Davide.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 121 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 8
27 Yesu akuchokera kumeneko, amuna awiri amene anali ndi vuto losaona+ anamutsatira akufuula kuti: “Mutichitire chifundo, Mwana wa Davide.”