Mateyu 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu atalowa mʼnyumba, amuna amene anali ndi vuto losaona aja anabwera kwa iye, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi mukukhulupirira kuti ndingachite zimenezi?”+ Iwo anamuyankha kuti: “Inde, Ambuye.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:28 Yesu—Ndi Njira, tsa. 121 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 8
28 Yesu atalowa mʼnyumba, amuna amene anali ndi vuto losaona aja anabwera kwa iye, ndipo anawafunsa kuti: “Kodi mukukhulupirira kuti ndingachite zimenezi?”+ Iwo anamuyankha kuti: “Inde, Ambuye.”