Mateyu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Iye ankaphunzitsa mʼmasunagoge awo komanso kulalikira uthenga wabwino wa Ufumu ndipo ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:35 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, tsa. 26
35 Ndiyeno Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Iye ankaphunzitsa mʼmasunagoge awo komanso kulalikira uthenga wabwino wa Ufumu ndipo ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+
9:35 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, tsa. 26