Mateyu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndikukuuzani, chilango cha mzinda umenewo chidzakhala chopweteka kwambiri pa Tsiku la Chiweruzo kuposa cha Sodomu ndi Gomora.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:15 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, ptsa. 30-317/15/1987, tsa. 27
15 Ndithu ndikukuuzani, chilango cha mzinda umenewo chidzakhala chopweteka kwambiri pa Tsiku la Chiweruzo kuposa cha Sodomu ndi Gomora.+