37 Aliyense amene amakonda kwambiri bambo ake kapena mayi ake kuposa ine ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga. Komanso aliyense amene amakonda kwambiri mwana wake wamwamuna kapena wamkazi kuposa ine ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga.+