Mateyu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yesu atamaliza kupereka malangizo kwa ophunzira ake 12 aja, anachoka kumeneko nʼkupita kukaphunzitsa ndi kukalalikira kumizinda ina.+
11 Yesu atamaliza kupereka malangizo kwa ophunzira ake 12 aja, anachoka kumeneko nʼkupita kukaphunzitsa ndi kukalalikira kumizinda ina.+