-
Mateyu 11:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Nanga munapita kukaona chiyani? Munthu wovala zovala zapamwamba kapena? Ayi, paja amene amavala zovala zapamwamba amapezeka mʼnyumba za mafumu.
-