Mateyu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nangano nʼchifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, Yohane ndi mneneri komanso ndi wofunika kwambiri kuposa aneneri.+
9 Nangano nʼchifukwa chiyani munapita makamaka? Kukaona mneneri kapena? Inde, ndikukuuzani, Yohane ndi mneneri komanso ndi wofunika kwambiri kuposa aneneri.+