Mateyu 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malemba amanena za iyeyu kuti: ‘Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga kuti atsogole kukakukonzera njira!’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 96 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 121/1/1987, tsa. 9
10 Malemba amanena za iyeyu kuti: ‘Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga kuti atsogole kukakukonzera njira!’+