Mateyu 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuyambira mʼmasiku a Yohane Mʼbatizi mpaka pano anthu akuyesetsa mwakhama kuti apeze mwayi wolowa mu Ufumu wakumwamba, ndipo amene akuyesetsa mwakhama akuupeza.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:12 Nsanja ya Olonda,2/1/2005, tsa. 117/15/1992, tsa. 18
12 Kuyambira mʼmasiku a Yohane Mʼbatizi mpaka pano anthu akuyesetsa mwakhama kuti apeze mwayi wolowa mu Ufumu wakumwamba, ndipo amene akuyesetsa mwakhama akuupeza.+