Mateyu 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mʼbadwo uwu ndiuyerekezere ndi ndani?+ Uli ngati ana aangʼono amene akhala pansi mʼmisika nʼkumafuulira anzawo amene amasewera nawo Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 98
16 Kodi mʼbadwo uwu ndiuyerekezere ndi ndani?+ Uli ngati ana aangʼono amene akhala pansi mʼmisika nʼkumafuulira anzawo amene amasewera nawo