Mateyu 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Tsoka kwa iwe Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida! Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli nʼkukhala paphulusa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:21 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, ptsa. 16-176/1/1988, tsa. 30
21 “Tsoka kwa iwe Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida! Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli nʼkukhala paphulusa.+