Mateyu 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma ndikukuuzani kuti chilango chanu chidzakhala chopweteka kwambiri kuposa cha Turo ndi Sidoni pa Tsiku la Chiweruzo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:22 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 30
22 Koma ndikukuuzani kuti chilango chanu chidzakhala chopweteka kwambiri kuposa cha Turo ndi Sidoni pa Tsiku la Chiweruzo.+