Mateyu 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa nthawi imeneyo Yesu ananena kuti: “Ndikukutamandani inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa anthu anzeru ndi ozindikira mwawabisira zinthu zimenezi ndipo mwaziulula kwa ana aangʼono.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:25 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 9
25 Pa nthawi imeneyo Yesu ananena kuti: “Ndikukutamandani inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa anthu anzeru ndi ozindikira mwawabisira zinthu zimenezi ndipo mwaziulula kwa ana aangʼono.+