Mateyu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi ina, Yesu ankadutsa mʼminda ya tirigu pa tsiku la Sabata. Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu nʼkumadya.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 76 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 281/15/1987, tsa. 22
12 Pa nthawi ina, Yesu ankadutsa mʼminda ya tirigu pa tsiku la Sabata. Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu nʼkumadya.+