Mateyu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye analowa mʼnyumba ya Mulungu ndipo anadya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,*+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sankayenera kudya malinga ndi malamulo, koma ansembe okha.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 76 Nsanja ya Olonda,9/1/2002, tsa. 181/15/1987, ptsa. 22-23
4 Iye analowa mʼnyumba ya Mulungu ndipo anadya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,*+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sankayenera kudya malinga ndi malamulo, koma ansembe okha.+