Mateyu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawayankha kuti: “Mutakhala ndi nkhosa imodzi yokha, ndiyeno nkhosayo nʼkugwera mʼdzenje pa tsiku la Sabata, kodi alipo pakati panu amene sangaigwire nʼkuitulutsa?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:11 Yesu—Ndi Njira, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,8/1/1998, ptsa. 9-101/1/1987, tsa. 15
11 Koma iye anawayankha kuti: “Mutakhala ndi nkhosa imodzi yokha, ndiyeno nkhosayo nʼkugwera mʼdzenje pa tsiku la Sabata, kodi alipo pakati panu amene sangaigwire nʼkuitulutsa?+