-
Mateyu 12:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako anauza munthuyo kuti: “Tambasula dzanja lako.” Iye analitambasuladi ndipo linakhalanso bwinobwino ngati linzake.
-