Mateyu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesu atadziwa zimenezi, anachoka pamalo amenewo. Anthu ambiri anamutsatira+ ndipo iye anawachiritsa onsewo,
15 Yesu atadziwa zimenezi, anachoka pamalo amenewo. Anthu ambiri anamutsatira+ ndipo iye anawachiritsa onsewo,