Mateyu 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Sadzakangana ndi munthu+ kapena kufuula ndipo palibe amene adzamve mawu ake mʼmisewu ikuluikulu. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:19 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 80-81