-
Mateyu 12:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Atadziwa maganizo awo, iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha ndipo mzinda kapena nyumba iliyonse yogawanika sikhalitsa.
-