-
Mateyu 12:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Komanso ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu za Belezebule, nanga otsatira anu amazitulutsa ndi mphamvu za ndani? Nʼchifukwa chake otsatira anuwo adzakuweruzani kuti ndinu olakwa.
-