-
Mateyu 12:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Kapena munthu angalowe bwanji mʼnyumba ya munthu wamphamvu nʼkumulanda katundu wake, ngati choyamba atapanda kumanga munthu wamphamvuyo? Akatero mʼpamene angathe kutenga katundu mʼnyumbamo.
-