Mateyu 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula mawu onyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, mʼnthawi* ino kapena ikubwerayo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 103 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, ptsa. 9-108/1/1987, tsa. 27 Kukambitsirana, ptsa. 343, 396-397
32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula mawu onyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, mʼnthawi* ino kapena ikubwerayo.+
12:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 103 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, ptsa. 9-108/1/1987, tsa. 27 Kukambitsirana, ptsa. 343, 396-397